1
DEUTERONOMO 20:4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye wakumuka nanu, kugwirira inu pa adani anu, kukupulumutsani.
Compare
Explore DEUTERONOMO 20:4
2
DEUTERONOMO 20:1
Pamene mutuluka pa mdani wanu kunkhondo, ndi kuona akavalo ndi magaleta ndi anthu akuchulukira inu, musawaopa; popeza Yehova Mulungu wanu, amene anakukwezani kukutulutsani m'dziko la Ejipito, ali ndi inu.
Explore DEUTERONOMO 20:1
3
DEUTERONOMO 20:3
nati nao, Tamverani, Israele, muyandikiza kunkhondo lero pa adani anu; musafumuka mitima yanu; musachita mantha, kapena kunjenjemera, kapena kuopsedwa pamaso pao
Explore DEUTERONOMO 20:3
Home
Bible
Plans
Videos