1
2 MBIRI 26:5
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo iye anali munthu wakufuna Mulungu masiku a Zekariya, ndiye wozindikira masomphenya a Mulungu; ndipo masiku akufunira Yehova iye, Mulungu anamlemereza
Compare
Explore 2 MBIRI 26:5
2
2 MBIRI 26:16
Koma atakhala wamphamvu, mtima wake unakwezeka momuononga, nalakwira Yehova Mulungu wake; popeza analowa m'Kachisi wa Yehova kufukiza pa guwa la nsembe la chofukiza.
Explore 2 MBIRI 26:16
Home
Bible
Plans
Videos