1
1 MAFUMU 8:56
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Wolemekezeka ndi Yehova amene anapumulitsa anthu ake Aisraele, monga mwa zonse analonjezazo; sanatayike mau amodzi a mau ake onse abwino, amene analankhula ndi dzanja la Mose mtumiki wake.
Compare
Explore 1 MAFUMU 8:56
2
1 MAFUMU 8:23
Yehova Mulungu wa Israele, palibe Mulungu wolingana ndi Inu m'thambo la kumwamba, kapena pa dziko lapansi, wakusungira chipangano ndi chifundo akapolo anu akuyenda ndi mtima wonse pamaso panu
Explore 1 MAFUMU 8:23
Home
Bible
Plans
Videos