1
Luka 10:19
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Ine ndakupatsani ulamuliro woponda njoka ndi zinkhanira, ndi kugonjetsa mphamvu zonse za mdani; palibe chimene chidzakupwetekani.
Compare
Explore Luka 10:19
2
Luka 10:41-42
Ambuye anati, “Marita, Marita, ukudandaula ndi kuvutika ndi zinthu zambiri, koma chofunika nʼchimodzi chokha. Mariya wasankha chinthu chabwino, ndipo palibe angamulande chimenechi.”
Explore Luka 10:41-42
3
Luka 10:27
Iye anayankha kuti, “Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse, ndi mphamvu zako zonse ndi nzeru zako zonse, ndi kukonda mnansi wako monga iwe mwini.”
Explore Luka 10:27
4
Luka 10:2
Iye anawawuza kuti, “Zokolola ndi zambiri, koma ogwira ntchito ndi ochepa. Pemphani Ambuye wa zokolola, kuti atumize antchito ku munda wake wa zokolola.
Explore Luka 10:2
5
Luka 10:36-37
“Kodi ukuganiza ndi ndani mwa atatuwa, amene anali mnansi wa munthu amene anavulazidwa ndi achifwambawo?” Katswiri wa Malamulo uja anayankha kuti, “Amene anamuchitira chifundo.” Yesu anamuwuza kuti, “Pita, uzikachita chimodzimodzi.”
Explore Luka 10:36-37
6
Luka 10:3
Pitani! Ine ndikukutumizani ngati nkhosa pakati pa mimbulu.
Explore Luka 10:3
Home
Bible
Plans
Videos