1
Machitidwe a Atumwi 10:34-35
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Ndipo Petro anayamba kuyankhula nati, “Zoonadi, tsopano ndazindikira kuti Mulungu sakondera. Koma amalandira anthu a mtundu uli wonse amene amaopa Iye ndiponso kuchita chilungamo.
Compare
Explore Machitidwe a Atumwi 10:34-35
2
Machitidwe a Atumwi 10:43
Aneneri onse achitira Iye umboni kuti aliyense amene akhulupirira Iye amakhululukidwa machimo chifukwa cha dzina lake.”
Explore Machitidwe a Atumwi 10:43
Home
Bible
Plans
Videos