1
MACHITIDWE 12:5
Buku Lopatulika
Pamenepo ndipo Petro anasungika m'ndende; koma Mpingo anampempherera iye kwa Mulungu kosalekeza.
Compare
Explore MACHITIDWE 12:5
2
MACHITIDWE 12:7
Ndipo taonani, mngelo wa Ambuye anaimirirapo, ndipo kuunika kunawala mokhalamo iye; ndipo anakhoma Petro m'nthiti, namuutsa iye, nanena, Tauka msanga. Ndipo maunyolo anagwa kuchoka m'manja mwake.
Explore MACHITIDWE 12:7
Home
Bible
Plans
Videos