Genesis 39:20-21

Genesis 39:20-21 CCL

Tsono iye anatenga Yosefe namuyika mʼndende mmene ankasungiramo amʼndende a mfumu. Ndipo Yosefe anakhala mʼndendemo koma Yehova anali naye, ndipo anamuonetsa kukoma mtima kwake, kotero kuti woyangʼanira ndende anakondwera ndi Yosefe.

ቪዲዮ ለ {{ዋቢ_ሰዉ}}